6 Ndipo anati, Tamvani tsono mau anga; pakakhala mneneri pakati pa inu, Ine Yehova ndidzizindikiritsa kwa iye m'masomphenya, ndinena naye m'kulota.
Werengani mutu wathunthu Numeri 12
Onani Numeri 12:6 nkhani