11 Wa pfuko la Yosefe, wa pfuko la Manase, Gadi mwana wa Susi.
12 Wa pfuko la Dani, Amiyeli mwana wa Gemali.
13 Wa pfuko la Aseri, Setri mwana wa Mikayeli.
14 Wa pfuko la Nafitali, Nabi mwana wa Vopisi.
15 Wa pfuko la Gadi, Geyuelimwana wa Maki.
16 Awandi maina a amunawo Mose anawatumira azonde dziko. Ndipo Mose anamucha Hoseya mwana wa Nuni Yoswa.
17 Potero Mose anawatuma azonde dziko la Kanani, nanena nao, Kwerani uko kumwela, nimukwere kumapiri;