23 Ndipo anadza ku cigwa ca Esikolo, nacekako tsango limodzi la mphesa, nalisenza awiri mopika; anabwera nazonso makangaza ndi nkhuyu.
Werengani mutu wathunthu Numeri 13
Onani Numeri 13:23 nkhani