27 Ndipo anafotokozera, nati, Tinakafika ku dziko limene munatitumirako, ndilo ndithu a moyenda mkaka ndi uci ngati madzi; ndi zipatso zace siizi.
Werengani mutu wathunthu Numeri 13
Onani Numeri 13:27 nkhani