Numeri 14:19 BL92

19 Khululukiranitu mphulupulu ya anthu awa, monga mwa cifundo canu cacikuru, ndi monga mudalekerera anthu awa, kuyambira Aigupto kufikira tsopano.

Werengani mutu wathunthu Numeri 14

Onani Numeri 14:19 nkhani