Numeri 14:2 BL92

2 Ndipo ana onse a Israyeli anadandaulira Mose ndi Aroni; ndi khamu lonse linanena nao, Mwenzi tikadafa m'dziko la Aigupto; kapena mwenzi tikadafa m'cipululu muno!

Werengani mutu wathunthu Numeri 14

Onani Numeri 14:2 nkhani