Numeri 14:22 BL92

22 popeza anthu onse awa amene adaona ulemerero wanga, ndi zizindikilo zanga, ndidazicita m'Aigupto ndi m'cipululu, koma anandiyesa Ine kakhumi aka, osamvera mau anga;

Werengani mutu wathunthu Numeri 14

Onani Numeri 14:22 nkhani