40 Ndipo anauka mamawa, nakwera pamwamba pa, phiri, nati, Tiri pano, tidzakwera kumka ku malo amene Yehova ananena; popeza tacimwa.
Werengani mutu wathunthu Numeri 14
Onani Numeri 14:40 nkhani