Numeri 15:14 BL92

14 Ndipo akakhala nanu mlendo, kapena ali yense wakukhala pakati pa inu mwa mibadwo yanu, nakacitira Yehova nsembe yamoto ya pfungo lokoma; monga mucita inu, momwemo iyenso,

Werengani mutu wathunthu Numeri 15

Onani Numeri 15:14 nkhani