Numeri 15:20 BL92

20 Pa mtanda wanu woyamba muperekeko kamtanda, kakhale nsembe yokweza; monga mumacitira nsembe yokweza ya popuntha tirigu, momwemo muzikakweza.

Werengani mutu wathunthu Numeri 15

Onani Numeri 15:20 nkhani