26 Ndipo khamu lonse la ana a Israyeli, adzakhululukidwa, ndi mlendo yemwe wakukhala pakati pao; popeza khamu lonse linacicita osati dala.
Werengani mutu wathunthu Numeri 15
Onani Numeri 15:26 nkhani