33 Ndipo amene adampezawo alinkufuna nkhuni anabwera naye kwa Mose ndi Aroni, ndi kwa khamu lonse.
Werengani mutu wathunthu Numeri 15
Onani Numeri 15:33 nkhani