38 Nena ndi ana a Israyeli, nuwauze kuti adziombere mphonje m'mphepete mwa zobvala zao, mwa mibadwo yao, naike pamphonje m'mphepetemo thonje lamadzi.
Werengani mutu wathunthu Numeri 15
Onani Numeri 15:38 nkhani