26 Ndipo ananena ndi khamulo, nati, Cokanitu ku mahema a anthu awa oipa, musamakhudza kanthu kao kali konse, mungaonongeke m'zocimwa zao zonse.
Werengani mutu wathunthu Numeri 16
Onani Numeri 16:26 nkhani