Numeri 16:34 BL92

34 Ndipo Aisrayeli onse akukhala pozinga pao anathawa pakumva kupfuula kwao; pakuti anati, Lingatimeze dziko ifenso.

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:34 nkhani