9 Ndipo Mose anaturutsa ndodo zonse kuzicotsa pamaso pa Yehova, azione ana onse a Israyeli; ndipo anapenya, natenga yense ndodo yace.
Werengani mutu wathunthu Numeri 17
Onani Numeri 17:9 nkhani