13 Zipatso zoyamba zonse ziri m'dziko mwao, zimene amadza nazo kwa Yehova, zikhale zako; oyera onse a m'banja lako adyeko.
Werengani mutu wathunthu Numeri 18
Onani Numeri 18:13 nkhani