22 Ndipo ciri conse munthu wodetsedwa acikhudza cidzakhala codetsedwa; ndi munthu wakucikhudza adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.
Werengani mutu wathunthu Numeri 19
Onani Numeri 19:22 nkhani