Numeri 2:12 BL92

12 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a pfuko la Simeoni; ndi kalonga wa ana a Simeoni ndiye Selumiyeli mwana wa Surisadai.

Werengani mutu wathunthu Numeri 2

Onani Numeri 2:12 nkhani