Numeri 2:27 BL92

27 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a pfuko la Aseri; ndi kalonga wa ana a Aseri ndiye Pagiyeli mwana wa Okirani.

Werengani mutu wathunthu Numeri 2

Onani Numeri 2:27 nkhani