5 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a pfuko la Isakara; ndipo kalonga wa ana a Isakara ndiye Netandi mwana wa Zuwara.
Werengani mutu wathunthu Numeri 2
Onani Numeri 2:5 nkhani