11 Ndipo Mose anasamula dzanja lace, napanda thanthwe kawiri ndi ndodo; ndipo madzi anaturukamo ocuruka, ndi khamulo linamwa, ndi zoweta zao zomwe.
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:11 nkhani