14 Pamenepo Mose anatumiza amithenga ocokera ku Kadesi kumuka kwa mfumu ya Edomu, ndi kuti, Atero mbale wanu Israyeli, Mudziwa zowawa zonse zinatigwera;
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:14 nkhani