16 Pamenepo tinapfuulira kwa Yehova, ndipo anamva mau athu, natuma mthenga, natiturutsa m'Aigupto; ndipo, taonani, tiri m'Kadesi, ndiwo mudzi wa malekezero a malire anu.
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:16 nkhani