22 Ndipo anayenda ulendo kucokera ku Kadesi; ndi ana a Israyeli, ndilo khamu lonse, anadza ku phiri la Hori.
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:22 nkhani