24 Aroni adzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wace; pakuti sadzalowa m'dziko limene ndapatsa ana a Israyeli, popeza munapikisana ndi mau anga ku madzi a Meriba.
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:24 nkhani