26 nubvule Aroni zobvala zace, numbveke Eleazara mwana wace; ndipo Aroni adzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wace, nadzafa komweko.
Werengani mutu wathunthu Numeri 20
Onani Numeri 20:26 nkhani