Numeri 20:29 BL92

29 Pamene khamu lonse linaona kuti Aroni adamwalira, anamlira Aroni masiku makumi atatu, ndiyo mbumba yonse ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 20

Onani Numeri 20:29 nkhani