Numeri 20:6 BL92

6 Ndipo Mose ndi Aroni anacoka pamaso pa msonkhano kumka ku khomo la cihema cokomanako, nagwa nkhope zao pansi; ndipo ulemerero wa Yehova unaonekera iwo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 20

Onani Numeri 20:6 nkhani