26 Popeza Hesiboni ndiwo mudzi wa Sihoni mfumu ya Aamori, imene idathira nkhondo pa mfumu idafayo ya Moabu, nilanda dziko lace m'dzanja lace kufikira Arinoni.
Werengani mutu wathunthu Numeri 21
Onani Numeri 21:26 nkhani