Numeri 21:33 BL92

33 Ndipo anatembenuka nakwera kudzera njira ya ku Basanu; ndipo Ogi mfumu ya ku Basana anaturuka kukumana nao, iye ndi anthu ace onse, kudzacita nao nkhondo ku Edreyi.

Werengani mutu wathunthu Numeri 21

Onani Numeri 21:33 nkhani