4 Ndipo anayenda ulendo kucokera ku phiri la Hori, nadzera njira ya Nyanja Yofiira, kupaza ku dziko la Edomu; ndi mtima wa anthu unada cifukwa ca njirayo.
Werengani mutu wathunthu Numeri 21
Onani Numeri 21:4 nkhani