Numeri 22:38 BL92

38 Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndiri nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:38 nkhani