16 Anenetsa wakumva mau a Mulungu,Ndi kudziwa nzeru ya Wam'mwambamwamba,Wakuona masomphenya a Wamphamvuyonse,Wakugwa pansi wopenyuka maso;
Werengani mutu wathunthu Numeri 24
Onani Numeri 24:16 nkhani