20 Ndipo anayang'ana ku Amaleki, nanena fanizo lace, nati,Amaleki ndiye woyamba wa amitundu;Koma citsiriziro cace, adzaonongeka ku nthawi zonse.
Werengani mutu wathunthu Numeri 24
Onani Numeri 24:20 nkhani