Numeri 25:4 BL92

4 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Gwira akuru onse a anthu nuwapacikire Yehova, pali dzuwa poyera, kuti mkwiyo waukali wa Yehova ucoke kwa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Numeri 25

Onani Numeri 25:4 nkhani