2 Werenga khamu lonse la ana a Israyeli, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, monga mwa nyumba za makolo ao, onse akuturukira kunkhondo m'Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Numeri 26
Onani Numeri 26:2 nkhani