Numeri 26:25 BL92

25 Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:25 nkhani