Numeri 26:33 BL92

33 Ndipo Tselofekadi mwana wa Heferi analibe ana amuna, koma ana akazi ndiwo; ndipo maina a ana akazi a Tselofekadi ndiwo Mala ndi Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:33 nkhani