Numeri 26:37 BL92

37 Iwo ndiwo mabanja a ana a Efraimu monga mwa owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi atatu mphambu ziwiri kudza mazana asanu. Iwo ndiwo ana amuna a Yosefe monga mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:37 nkhani