Numeri 26:42 BL92

42 Mwana wamwamuna wa Dani monga mwa mabanja ace ndiye Suhamu, ndiye kholo la banja la Asuhamu. Iwo ndiwo mabanja a Dani monga mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:42 nkhani