Numeri 26:44 BL92

44 Ana amuna a Aseri monga mwa mabanja ao ndiwo: Yimna, ndiye kholo la banja la Ayimna; Yisivi, ndiye kholo la banja la Ayisivi; Beriya, ndiye kholo la banja la Aberiya.

Werengani mutu wathunthu Numeri 26

Onani Numeri 26:44 nkhani