Numeri 28:8 BL92

8 Ndi mwana wa nkhosa winayo umpereke madzulo; monga nsembe yaufa ya m'mawa, ndi nsembe yothira yace, umpereke; ndiyo nsembe yamoto ya pfungo lokoma la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Numeri 28

Onani Numeri 28:8 nkhani