Numeri 29:21 BL92

21 ndi nsembe yace yaufa, ndi nsembe zace zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za ana a nkhosa monga mwa kuwerenga kwace, ndi kutsata lemba lace;

Werengani mutu wathunthu Numeri 29

Onani Numeri 29:21 nkhani