Numeri 29:3 BL92

3 ndi nsembe yao yaufa, ufa wosalala wosanganiza ndi mafuta, atatu a magawo khumi akhale a ng'ombeyo, awiri a magawo khumi akhale a nkhosa yamphongo,

Werengani mutu wathunthu Numeri 29

Onani Numeri 29:3 nkhani