Numeri 29:33 BL92

33 ndi nsembe yace yaufa, ndi nsembe zace zothira, za ng'ombe, za nkhosa yamphongo, ndi za ana a nkhosa, monga mwa kuwerenga kwace, ndi kutsata lemba lace;

Werengani mutu wathunthu Numeri 29

Onani Numeri 29:33 nkhani