Numeri 3:45 BL92

45 Landira Alevi m'malo mwa oyamba kubadwa onse mwa ana a Israyeli, ndi ng'ombe za Alevi m'malo mwa ng'ombe zao; ndipo Alevi azikhala anga; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Numeri 3

Onani Numeri 3:45 nkhani