23 zonse zakulola moto, mupititse m'moto, ndipo zidzakhala zoyera; koma muziyeretsenso ndi madzi akusiyanitsa. Koma zonse zosalola moto, muzipititse m'madzi.
Werengani mutu wathunthu Numeri 31
Onani Numeri 31:23 nkhani