15 Pakuti mukabwerera m'mbuyo kusamtsata iye, adzawasiyanso m'cipululu, ndipo mudzaononga anthu awa onse.
Werengani mutu wathunthu Numeri 32
Onani Numeri 32:15 nkhani