23 Koma mukapanda kutero, taonani, mwacimwira Yehova; ndipo zindikirani kuti cimo lanu lidzakupezani.
Werengani mutu wathunthu Numeri 32
Onani Numeri 32:23 nkhani